Psalms 46:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kuli mtsinje umene mifuleni yake imasangalatsa anthu amumzinda wa Mulungu, malo oyera okhalako Wopambanazonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pali mtsinje, ngalande zake zidzakondweretsa mudzi wa Mulungu. Malo oyera okhalamo Wam'mwambamwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuli mtsinje umene njira zake za madzi zimasangalatsa mzinda wa Mulungu, malo oyera kumene Wammwambamwamba amakhalako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pali mtsinje, ngalande zace zidzakondweretsa mudzi wa Mulungu. Malo oyera okhalamo Wam'mwambamwamba,