Psalms 46:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu ali m'kati mwa mzindawo, sudzaonongeka konse. Mulungu adzauthandiza dzuŵa lisanatuluke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu ali m'kati mwake, sudzasunthika, Mulungu adzauthandiza mbandakucha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu ali mʼkati mwake, iwo sudzagwa; Mulungu adzawuthandiza mmawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu ali m'kati mwace, sudzasunthika: Mulungu adzauthandiza mbanda kuca.