Psalms 46:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitundu ya anthu ikunjenjemera kwambiri, maufumu akugwedezeka, Mulungu akalankhula mau ake, dziko lapansi likusungunuka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amitundu anapokosera, maufumu anagwedezeka, ananena mau, dziko lapansi linasungunuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitundu ikupokosera, mafumu akugwa; Iye wakweza mawu ake, dziko lapansi likusungunuka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amitundu anapokosera; maufumu anagwedezeka: Ananena mau, dziko lapansi linasungunuka.