Psalms 46:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwerani kuti muwone ntchito za Chauta, m'mene amachitira zozizwitsa pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Idzani, penyani ntchito za Yehova, amene achita zopululutsa pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bwerani kuti mudzaone ntchito za Yehova, chiwonongeko chimene wachibweretsa pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Idzani, penyani nchito za Yehova, Amene acita zopululutsa pa dziko lapansi.