Psalms 46:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amaletsa nkhondo mpaka ku mathero a dziko lapansi. Amathyola uta, ndi kupokonyola mkondo. Amatentha magaleta ankhondo ndi moto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aletsa nkhondo ku malekezero a dziko lapansi; athyola uta, nadula nthungo; atentha magaleta ndi moto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amathetsa nkhondo ku malekezero a dziko lapansi; Iye amathyola uta ndi kupindapinda mkondo; amatentha zishango ndi moto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aletsa nkhondo ku malekezero adziko lapansi; Athyola uta, nadula nthungo; Atentha magareta ndi moto.