Psalms 47:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adatigonjetsera anthu ambirimbiri, mitundu ina ya anthu adaiika pansi pa ulamuliro wathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atigonjetsera anthu, naika amitundu pansi pa mapazi athu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatigonjetsera mitundu yambirimbiri ya anthu; anayika anthu pansi pa mapazi athu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atigonjetsera anthu, Naika amitundu pansi pa mapazi athu.