Psalms 47:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatisankhulira dzikoli kuti likhale choloŵa chathu, adatipatsa ife anthu a Yakobe dziko lokomali pakuti amatikonda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atisankhira cholowa chathu, chokometsetsa cha Yakobo amene anamkonda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatisankhira cholowa chathu, chonyaditsa cha Yakobo, amene anamukonda. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atisankhira colowa cathu, Cokometsetsa ca Yakobo amene anamkonda.