Psalms 47:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu wakwera, anthu akumfuulira, Chauta wakwera, akumuimbira lipenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu wakwera ndi mfuu, Yehova ndi liu la lipenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu wakwera, anthu akumufuwulira mwachimwemwe, Yehova wakwera, akumuyimbira malipenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu wakwera ndi mpfuu, Yehova ndi liu la lipenga.