Psalms 47:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu amalamulira mitundu ya anthu. Mulungu amakhala pa mpando wake woyera waufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu ndiye mfumu ya amitundu, Mulungu akhala pa mpando wachifumu wake woyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu akulamulira mitundu ya anthu; Mulungu wakhala pa mpando wake waufumu woyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu ndiye Mfumu ya amitundu: Mulungu akhala pa mpando wacifumu wace woyera.