Psalms 48:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, anthu amakutamandani ponseponse, monga dzina lanu latchuka pa dziko lonse lapansi. Dzanja lanu lamphamvu limapambana nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga dzina lanu, Mulungu, momwemo lemekezo lanu ku malekezero a dziko lapansi; m'dzanja lamanja lanu mudzala chilungamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga dzina lanu, Inu Mulungu, matamando anu amafika ku malekezero a dziko lapansi dzanja lanu lamanja ladzaza ndi chilungamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga dzina lanu, Mulungu, Momwemo lemekezo lanu ku malekezero a dziko lapansi: M'dzanja lamanja lanu mudzala cilungamo.