Psalms 48:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu okhala mu Ziyoni akondwe. A ku Yuda asangalale chifukwa cha kaweruzidwe kanu kolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Likondwere phiri la Ziyoni, asekere ana akazi a Yuda, chifukwa cha maweruzo anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Phiri la Ziyoni likukondwera, midzi ya Yuda ndi yosangalala chifukwa cha maweruzo anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Likondwere phiri la Ziyoni, Asekere ana akazi a Yuda, Cifukwa ca maweruzo anu.