Psalms 48:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mzinda wokongola wa Ziyoni pa phiri la Mulungu, wopatsa chimwemwe ku dziko lonse lapansi. Mzinda wa Ziyoni umene uli kumpotowu, ndi mzinda wa Mfumu yathu yaikulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Phiri la Ziyoni, chikhalidwe chake nchokoma kumbali zake za kumpoto, ndilo chimwemwe cha dziko lonse lapansi, mudzi wa mfumu yaikulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lokongola mu utali mwake, chimwemwe cha dziko lonse lapansi. Malo aatali kwambiri a Zafoni ndiye Phiri la Ziyoni, mzinda wa Mfumu yayikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Phiri la Ziyoni, cikhalidwe cace ncokoma Ku mbali zace za kumpoto, Ndilo cimwemwe ca dziko lonse lapansi, Mudzi wa mfumu yaikuru.