Psalms 48:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanjenjemera koopsa, ndipo adamva ululu wonga wa mkazi wovutika pa nthaŵi yochira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo anagwidwa nako kunthunthumira; anamva chowawa, ngati wam'chikuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pomwepo anagwidwa nako kunjenjemera, ululu wonga wa mkazi woyembekezera pa nthawi yochira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomwepo anagwidwa nako kunthunthumira; Anamva cowawa, ngati wam'cikuta.