Psalms 48:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimene ife tidazimva, taziwona zomwezo mu mzinda wa Chauta Wamphamvuzonse, mzinda wa Mulungu wathu, umene adaukhazikitsa mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga tidamva, momwemo tidapenya m'mudzi wa Yehova wa makamu, m'mudzi wa Mulungu wathu, Mulungu adzaukhazikitsa kunthawi yamuyaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga momwe tinamvera, kotero ife tinaona mu mzinda wa Yehova Wamphamvuzonse, mu mzinda wa Mulungu wathu. Mulungu adzawuteteza kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga tidamva, momwemo tidapenya M'mudzi wa Yehova wa makamu, m'mudzi wa Mulungu wathu: Mulungu adzaukhazikitsa ku nthawi yamuyaya.