Psalms 48:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tikakhala m'Nyumba mwanu, Inu Mulungu, timalingalira za chikondi chanu chosasinthika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tidalingalira zachifundo chanu, Mulungu, m'kati mwa Kachisi wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼkati mwa Nyumba yanu Mulungu, ife timalingaliramo zachikondi chanu chosasinthika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tidalingalira za cifundo canu, Mulungu, M'kati mwa Kacisi wanu.