Psalms 49:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Manda ao ndiye kwao mpaka muyaya, ndi malo odzakhalako pa mibadwo yonse, ngakhale akadali moyo ankatcha maiko maina ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mumtima mwao ayesa kuti nyumba zao zikhala chikhalire, ndi mokhala iwo ku mibadwomibadwo; atchapo dzina lao padziko pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Manda awo adzakhala nyumba zawo mpaka muyaya, malo awo okhalako kwa nthawi yonse ya mibado yawo, ngakhale anatchula malo mayina awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mumtima mwao ayesa kuti nyumba zao zikhala cikhalire, Ndi mokhala iwo ku mibadwo mibadwo; Achapo dzina lao padziko pao.