Psalms 49:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale munthu akhale wolemera chotani, komabe adzafa chabe ngati nyama zakuthengo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma munthu wa ulemu wake sakhalitsa, afanana ndi nyama za kuthengo, afanana nazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale munthu akhale wachuma chotani, adzafa ngati nyama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma munthu wa ulemu wace sakhalitsa: Afanana ndi nyama za kuthengo, afanana nazo.