Psalms 49:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi ndizo zimene zimaŵagwera anthu amene ali ndi chikhulupiriro chopusa, ndiwo mathero ake a onse amene amatsata maganizo otere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Njira yao yino ndiyo kupusa kwao, koma akudza m'mbuyo avomereza mau ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Izi ndi zimene zimachitikira iwo amene amadzidalira okha, ndi owatsatira awo amene amavomereza zimene amayankhula. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Njira yao yino ndiyo kupusa kwao: Koma akudza m'mbuyo abvomereza mau ao.