Psalms 49:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mulungu adzaombola moyo wanga ku ulamuliro wa manda, sindidzaopa, pakuti Iye adzandilandira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Mulungu adzaombola moyo wanga kumphamvu ya manda. Pakuti adzandilandira ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Mulungu adzawombola moyo wanga kuchoka ku manda; ndithu Iye adzanditengera kwa Iye mwini.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Mulungu adzaombola moyo wanga ku mphamvu ya manda: Pakuti adzandilandira ine.