Psalms 49:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale pamene munthuyo ali moyo, amadziyesa wodala, ndipo ngakhale atamandidwe pamene zinthu zikumuyendera bwino,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Angakhale anadalitsa moyo wake pokhala ndi moyo, ndipo anthu akulemekeza iwe, podzichitira wekha zokoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale pamene munthuyo ali moyo amadziyesa wodala, ndipo ngakhale atamandidwe pamene zinthu zikumuyendera bwino,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Angakhale anadalitsa moyo wace pokhala ndi moyo, Ndipo anthu akulemekeza iwe, podzicitira wekha zokoma,