Psalms 49:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
adzafabe nkukakumana ndi makolo ake onse kumanda, kumene sadzaona kuŵala mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzamuka kumbadwo wa makolo ake; sadzaona kuunika nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
iyeyo adzakakhala pamodzi ndi mʼbado wa makolo ake, amene sadzaonanso kuwala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzamuka ku mbadwo wa makolo ace; Sadzaona kuunika nthawi zonse.