Psalms 49:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale munthu akhale wolemera chotani, komabe akasoŵa nzeru, adzafa chabe ngati nyama zakuthengo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu waulemu, koma wosadziwitsa, afanana ndi nyama za kuthengo, afanana nazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu amene ali ndi chuma koma wopanda nzeru adzafa ngati nyama yakuthengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu waulemu, koma wosadziwitsa, Afanana ndi nyama za kuthengo, afanana nazo.