Psalms 49:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndichitirenji mantha pa nthaŵi yamavuto pamene anthu ondizunza akundizinga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzaoperanji masiku oipa, pondizinga amphulupulu onditsata kuchidendene?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndichitirenji mantha pamene masiku oyipa afika, pamene achinyengo oyipa andizungulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzaoperanji masiku oipa, Pondizinga amphulupulu onditsata kucidendene?