Psalms 49:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu otero amangokhulupirira chuma chao, amanyada chifukwa ali ndi chuma chambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo akutama kulemera kwao; nadzitamandira pa kuchuluka kwa chuma chao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amene adalira kulemera kwawo ndi kutamandira kuchuluka kwa chuma chawo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo akutama kulemera kwao; Nadzitamandira pa kucuruka kwa cuma cao;