Psalms 5:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imvani mau anga, Inu Chauta, mverani kusisima kwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo; aimbire zitoliro. Salimo la Davide. Mverani mau anga, Yehova, Zindikirani kulingirira kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe zoyimbira za zitoliro. Salimo la Davide. Tcherani khutu ku mawu anga, Inu Yehova, ganizirani za kusisima kwanga
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mverani mau anga, Yehova, Zindikirani kulingirira kwanga.