Psalms 5:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Asenzetseni tchimo lao, Inu Mulungu. Upo wao woipa uŵagwetse iwo omwe, muŵachotse pamaso panu chifukwa cha zochimwa zao zambirimbiri, chifukwa akuukirani Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muwayese otsutsika Mulungu; agwe nao uphungu wao. M'kuchuluka kwa zolakwa zao muwapirikitse; pakuti anapikisana ndi Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lengezani kuti ndi olakwa, Inu Mulungu! Zochita zawo zoyipa zikhale kugwa kwawo. Achotseni pamaso panu chifukwa cha machimo awo ambiri, pakuti awukira Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muwayese otsutsika Mulungu; Agwe nao uphungu wao: M'kucuruka kwa zolakwa zao muwapitikitse; Pakuti anapikisana ndi Inu.