Psalms 5:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa, Inu Chauta, mumamva mau anga. M'maŵa ndimapemphera kwa Inu, ndi kudikira kuti mundiyankhe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mawa, Yehova, mudzamva mau anga; m'mawa, ndidzakukonzerani pemphero langa, ndipo ndidzadikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa, Yehova mumamva mawu anga; Mmawa ndimayala zopempha zanga pamaso panu ndi kudikira mwachiyembekezo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mawa, Yehova, mudzamva mau anga; M'mawa, ndidzakukonzerani pemphero langa, ndipo ndidzadikira.