Psalms 5:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mumaŵaononga anthu olankhula zonama. Inu Chauta mumanyansidwa nawo anthu onyenga ndi opha anzao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzaononga iwo akunena bodza; munthu wokhetsa mwazi ndi wachinyengo, Yehova anyansidwa naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mumawononga iwo amene amanena mabodza; anthu akupha ndi achinyengo, Yehova amanyansidwa nawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzaononga iwo akunena bodza: Munthu wokhetsa mwazi ndi wacinyengo, Yehova anyansidwa naye.