Psalms 50:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta, Mulungu Wamphamvu uja, akulankhula, akuitana anthu a ku dziko lonse lapansi, kuyambira kotulukira dzuŵa mpaka koloŵera kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo la Asafu. Mulungu wa milungu, Yehova, wanena, aitana dziko lapansi kuyambira kutuluka kwa dzuwa kufikira kulowa kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Asafu. Wamphamvuyo, Yehova Mulungu, akuyankhula ndi kuyitanitsa dziko lapansi kuyambira kotulukira dzuwa mpaka kumene limalowera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu wa milungu, Yehova, wanena, Aitana dziko lapansi kuyambira kuturuka kwa dzuwa kufikira kulowa kwace.