Psalms 50:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ndimadya nyama yang'ombe kapena magazi ambuzi?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi ndidzadya nyama ya ng'ombe, kapena kumwa mwazi wa mbuzi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndimadya nyama ya ngʼombe zazimuna kapena kumwa magazi a mbuzi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi ndidzadya nyama ya ng'ombe, Kapena kumwa mwazi wa mbuzi?