Psalms 50:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kwa munthu woipa Mulungu amati, “Ukuvutikiranji ndi kutchula malamulo anga? Bwanji pakamwa pako pakulankhula za chipangano changa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kwa woipa Mulungu anena, Uli nao chiyani malemba anga kulalikira, ndi kutchula pangano langa pakamwa pako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma kwa woyipa, Mulungu akuti, “Kodi uli ndi mphamvu yanji kuti uzinena malamulo anga kapena kutenga pangano langa pa milomo yako?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kwa woipa Mulungu anena, Uli nao ciani malemba anga kulalikira, Ndi kuchula pangano langa pakamwa pako?