Psalms 50:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe sufuna kulangizidwa, umaponya mau anga ku nkhongo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza udana nacho chilangizo, nufulatira mau anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe umadana ndi malangizo anga ndipo umaponyera kumbuyo kwako mawu anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza udana naco cilangizo, Nufulatira mau anga.