Psalms 50:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Umakhala pansi nkumachitira mbale wako miseche, inde, umasinjirira mbale wako weniweni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ukhala, nuneneza mbale wako; usinjirira mwana wa mai wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi zonse umayankhula motsutsana ndi mʼbale wako ndipo umasinjirira mwana wa amayi ako enieni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukhala, nuneneza mbale wako; Usinjirira mwana wa mai wako.