Psalms 50:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amaitana zamumlengalenga ndi za pansi pano, kuti zichite umboni pamene akuweruza anthu ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumwamba adzaitana zakumwamba, ndi dziko lapansi, kuti aweruze anthu ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye akuyitanitsa zamumlengalenga ndi za pa dziko lapansi kuti aweruze anthu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumwamba adzaitana zakumwamba, Ndi dziko lapansi, kuti aweruze anthu ace: