Psalms 50:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye akuti, “Sonkhanitsani pamaso panga, anthu anga okhulupirika, amene adachita chipangano ndi Ine popereka nsembe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundisonkhanitsire okondedwa anga; amene anapangana ndi Ine ndi nsembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mundisonkhanitsire okhulupirika anga, amene anachita pangano ndi ine pochita nsembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundisonkhanitsire okondedwa anga; Amene anapangana ndi Ine ndi nsembe.