Psalms 51:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muŵachitire zabwino anthu a ku Ziyoni, chifukwa cha kukoma mtima kwanu. Mumangenso kachiŵiri makoma a Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chitirani Ziyoni chokoma monga mwa kukondwera kwanu; mumange malinga a miyala a Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa kukoma mtima kwanu mupange Ziyoni kuti alemere; mumange makoma a Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Citirani Ziyoni cokoma monga mwa kukondwera kwanu; Mumange malinga a miyala a Yerusalemu.