Psalms 51:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zolakwa zanga ndikuzidziŵa, kuchimwa kwanga ndikukuzindikira nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa ndazindikira machimo anga; ndipo choipa changa chili pamaso panga chikhalire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndikudziwa mphulupulu zanga, ndipo tchimo langa lili pamaso panga nthawi zonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ndazindikira macimo anga; Ndipo coipa canga ciri pamaso panga cikhalire: