Psalms 52:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwanji ukunyadira ntchito zako zoipa, munthu wamphamvuwe?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo; Chilangizo cha Davide. Muja analowa Doegi Mwedomu nauza Saulo nati kwa iye, Davide walowa m'nyumba ya Ahimeleki. Udzitamandiranji ndi choipa, chiphona iwe? Chifundo cha Mulungu chikhala tsiku lonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe, ndakatulo ya Davide; pamene Doegi Mwedomu anapita kwa Sauli ndi kunena kuti “Davide wapita ku nyumba ya Ahimeleki.” Nʼchifukwa chiyani ukudzitamandira ndi zoyipa, iwe munthu wamphamvu? Nʼchifukwa chiyani ukudzitamandira tsiku lonse, iwe munthu wochititsa manyazi pamaso pa Mulungu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Udzitamandiranji ndi coipa, ciphonaiwe? Cifundo ca Mulungu cikhala tsiku lonse.