Psalms 52:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mulungu adzakutswanya kosalekeza, adzakugwira ndi kukutulutsira kunja kwa nyumba yako. Adzakuzula m'dziko la anthu amoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero Mulungu adzakupasula kunthawi zonse, adzakuchotsa nadzakukwatula m'hema mwako, nadzakuzula, kukuchotsa m'dziko la amoyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zoonadi Mulungu adzakutsitsa kupita ku chiwonongeko chamuyaya: iye adzakukwatula ndi kukuchotsa mʼtenti yako; iye adzakuzula kuchoka mʼdziko la amoyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero Mulungu adzakupasula ku nthawi zonse, Adzakucotsa nadzakukwatula m'hema mwako, Nadzakuzula, kukucotsa m'dziko la amoyo.