Psalms 52:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ochita zachilungamo adzaona zimenezi, ndipo adzachita mantha. Adzakuseka ndi kumanena kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo olungama adzachiona, nadzaopa, nadzamseka, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Olungama adzaona zimenezi ndi kuchita mantha; adzamuseka nʼkumanena kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo olungama adzaciona, nadzaopa, Nadzamseka, ndi kuti,