Psalms 52:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Muwoneni munthu amene sadafune kudalira Mulungu, koma adakhulupirira chuma chake chochuluka, nalimbikira kuchita zoipa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tapenyani, suyu munthuyu amene sanamuyese Mulungu mphamvu yake; amene anatama kuchuluka kwa chuma chake, nadzilimbitsa m'kuipsa kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pano tsopano pali munthu amene sanayese Mulungu linga lake, koma anakhulupirira chuma chake chambiri nalimbika kuchita zoyipa!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tapenyani, suyu munthuyu amene sanamuyesa Mulungu mphamvu yace; Amene anatama kucuruka kwa cuma cace, Nadzilimbitsa m'kuipsa kwace.