Psalms 52:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine ndili ngati mtengo wauŵisi wa olivi m'Nyumba ya Mulungu. Ndimaika mtima nthaŵi zonse pa chikondi chosasinthika cha Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine ndine ngati mtengo wauwisi wa azitona m'nyumba ya Mulungu. Ndikhulupirira chifundo cha Mulungu kunthawi za nthawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ine ndili ngati mtengo wa olivi wobiriwira bwino mʼnyumba ya Mulungu; ndimadalira chikondi chosatha cha Mulungu kwa nthawi za nthawi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine ndine ngati mtengo wauwisi waazitona m'nyumba ya Mulungu: Ndikhulupirira cifundo ca Mulungu ku nthawi za nthawi.