Psalms 53:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu kumwambako waŵerama, akuyang'ana anthu pansi pano, kuti aone ngati angakhalepo mmodzi wanzeru wofunitsitsa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu m'mwamba anaweramira pa ana a anthu, kuti aone ngati aliko wanzeru, wakufuna Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu kumwamba amayangʼana pansi pano pa ana a anthu kuti aone ngati alipo wina wanzeru, wofunafuna Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu m'mwamba anaweramira pa ana a anthu, Kuti aone ngati aliko wanzeru, Wakufuna Mulungu.