Psalms 53:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ai anthu onse ndi osokera, onsewo ndi oipa chimodzimodzi. Palibe ndi mmodzi yemwe wochita zabwino, ai, palibiretu ndi mmodzi yemwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onse anabwerera; anavunda mtima pamodzi; palibe mmodzi wakuchita bwino, nnena mmodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense wabwerera, iwo onse pamodzi akhala oyipa; palibe ndi mmodzi yemwe amene amachita chabwino, ngakhale mmodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onse anabwerera; anabvunda mtima pamodzi; Palibe mmodzi wakucita bwino, nnena mmodzi.