Psalms 54:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onyada andiwukira, anthu ankhalwe amafunafuna moyo wanga, iwo saganizako za Inu Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti alendo andiukira, ndipo oopsa afunafuna moyo wanga; sadziikira Mulungu pamaso pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Alendo akundithira nkhondo; anthu ankhanza akufunafuna moyo wanga, anthu amene salabadira za Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti alendo andiukira, Ndipo oopsa afunafuna moyo wanga; Sadziikira Mulungu pamaso pao.