Psalms 55:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, tcherani khutu kuti mumve pemphero langa, musabisale pamene ndikukupembani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Zirumbu. Chilangizo cha Davide. Tcherani khutu pemphero langa, Mulungu; ndipo musadzibisa pa kupemba kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Ndakatulo ya Davide. Pa zoyimbira za zingwe. Mvetserani pemphero langa, Inu Mulungu, musakufulatire kupempha kwanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cherani khutu pemphero langa, Mulungu; Ndipo musadzibisa pa kupemba kwanga.