Psalms 55:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usana ndi usiku iwo akuuzungulira pa makoma ake, mumzindamo muli chiwawa ndi nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Izizo ziuzungulira pa malinga ake usana ndi usiku; ndipo m'kati mwake muli zopanda pake ndi chovuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Usana ndi usiku iwo akuzungulirazungulira pa makoma ake; nkhwidzi ndi kuzunza kuli mʼkati mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Izizo ziuzungulira pa malinga ace usana ndi usiku; Ndipo m'kati mwace muli zapanda pace ndi cobvuta.