Psalms 55:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'menemo muli chiwonongeko chokhachokha. M'misika yake muli zopanikizana ndi zonyenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'kati mwake muli kusakaza, chiwawa ndi chinyengo sizichoka m'makwalala ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mphamvu zowononga zili pa ntchito mu mzinda; kuopseza ndi mabodza sizichoka mʼmisewu yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'kati mwace muli kusakaza: Ciwawa ndi cinyengo sizicoka m'makwalala ace.