Psalms 55:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma iweyo mnzanga, mnzanga woyenda naye, bwenzi langa wozoloŵerana naye, ndi amene ukuchita zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ameneyo ndiwe, munthu woyenerana nane, tsamwali wanga, wodziwana nane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma iweyo mnzanga, mnzanga woyenda naye, bwenzi langa la pondaapanʼpondepo, ndi amene ukuchita zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ameneyo ndiwe, munthu woyenerana nane, Tsamwali wanga, wodziwana nane.