Psalms 55:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tinkakambirana nkhani zokoma tili aŵiri, tinkapembedza limodzi m'Nyumba ya Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tinapangirana upo wokoma, tinaperekeza khamu la anthu popita kunyumba ya Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mnzanga amene nthawi ina tinkasangalala pa chiyanjano chokoma ku nyumba ya Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tinapangirana upo wokoma, Tinaperekeza khamu la anthu popita ku nyumba ya Mulungu.